Aefeso 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndithudi munamva kuti ndinaikidwa kukhala woyang’anira+ kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kuti ndikuthandizeni, Tito 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Mulungu waonetsa+ kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene kumabweretsa chipulumutso+ kwa anthu, kaya akhale a mtundu wotani.+
2 Ndithudi munamva kuti ndinaikidwa kukhala woyang’anira+ kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kuti ndikuthandizeni,
11 Pakuti Mulungu waonetsa+ kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene kumabweretsa chipulumutso+ kwa anthu, kaya akhale a mtundu wotani.+