Yohane 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo sali mbali ya dziko,+ monganso ine sindili mbali ya dziko.+ 1 Yohane 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musamakonde dziko kapena zinthu za m’dziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+
15 Musamakonde dziko kapena zinthu za m’dziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+