1 Akorinto 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti aliyense amene ali mwa Ambuye amene anaitanidwa ali kapolo ndi womasulidwa wa Ambuye,+ momwemonso amene anaitanidwa ali mfulu+ ndi kapolo+ wa Khristu. Agalatiya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi ndiye kuti tsopano ndikufuna kukopa anthu kapena Mulungu? Kapena kodi ndikungofuna kukondweretsa anthu?+ Ndikanakhala kuti ndikukondweretsabe anthu,+ sindikanakhala kapolo wa Khristu.+
22 Pakuti aliyense amene ali mwa Ambuye amene anaitanidwa ali kapolo ndi womasulidwa wa Ambuye,+ momwemonso amene anaitanidwa ali mfulu+ ndi kapolo+ wa Khristu.
10 Kodi ndiye kuti tsopano ndikufuna kukopa anthu kapena Mulungu? Kapena kodi ndikungofuna kukondweretsa anthu?+ Ndikanakhala kuti ndikukondweretsabe anthu,+ sindikanakhala kapolo wa Khristu.+