Aroma 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Si zokhazo, koma tiyeni tikondwere pamene tili m’masautso,+ popeza tikudziwa kuti chisautso chimabala chipiriro.+
3 Si zokhazo, koma tiyeni tikondwere pamene tili m’masautso,+ popeza tikudziwa kuti chisautso chimabala chipiriro.+