Luka 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano atumwiwo anauza Ambuye kuti: “Tiwonjezereni chikhulupiriro.”+ 1 Atesalonika 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso, Ambuye akuthandizeni kuti muwonjezereke,+ ndiponso kuti chikondi+ chanu kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse chikule.
12 Komanso, Ambuye akuthandizeni kuti muwonjezereke,+ ndiponso kuti chikondi+ chanu kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse chikule.