2 Akorinto 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti ngati ndinalankhula mokunyadirani kwa iyeyo, simunandichititse manyazi. Koma zimene tinalankhula monyadira kwa Tito n’zoona,+ monganso mmene zilili zinthu zonse zimene tinalankhula nanu. 1 Atesalonika 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?
14 Pakuti ngati ndinalankhula mokunyadirani kwa iyeyo, simunandichititse manyazi. Koma zimene tinalankhula monyadira kwa Tito n’zoona,+ monganso mmene zilili zinthu zonse zimene tinalankhula nanu.
19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?