1 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri, 1 Atesalonika 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Munatero chifukwa inunso munayamba kuvutitsidwa+ ndi anthu akwanu, ngati mmene iwonso akuvutitsidwira ndi Ayuda, 1 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipotu anakuitanirani ku moyo umenewu, pakuti ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+
6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri,
14 Pakuti inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Munatero chifukwa inunso munayamba kuvutitsidwa+ ndi anthu akwanu, ngati mmene iwonso akuvutitsidwira ndi Ayuda,
21 Ndipotu anakuitanirani ku moyo umenewu, pakuti ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+