Deuteronomo 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.+ 1 Akorinto 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti m’chilamulo cha Mose muli mawu akuti: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Kodi ndi ng’ombe zimene Mulungu akusamalira?
9 Pakuti m’chilamulo cha Mose muli mawu akuti: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Kodi ndi ng’ombe zimene Mulungu akusamalira?