Yeremiya 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mkwiyo wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake+ ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi ndipo mudzazimvetsa.+ Danieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+ Mateyu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+ Yuda 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 mmene anali kukuuzani kuti: “M’masiku otsiriza kudzakhala onyodola, otsatira zilakolako zawo pa zinthu zonyoza Mulungu.”+
20 Mkwiyo wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake+ ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi ndipo mudzazimvetsa.+
14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+
3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+
18 mmene anali kukuuzani kuti: “M’masiku otsiriza kudzakhala onyodola, otsatira zilakolako zawo pa zinthu zonyoza Mulungu.”+