Deuteronomo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Munthu akakhala ndi mwana wamwamuna wosamvera ndi wopanduka,+ amene samvera mawu a bambo ake kapena a mayi ake,+ ndipo amulangiza koma sawamvera,+ Miyambo 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Diso limene limanyoza bambo ake ndiponso limene silimvera mayi ake,+ akhwangwala a kuchigwa* adzalikolowola ndipo ana a chiwombankhanga adzalidya. Aefeso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,”+ ndilo lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo:+
18 “Munthu akakhala ndi mwana wamwamuna wosamvera ndi wopanduka,+ amene samvera mawu a bambo ake kapena a mayi ake,+ ndipo amulangiza koma sawamvera,+
17 Diso limene limanyoza bambo ake ndiponso limene silimvera mayi ake,+ akhwangwala a kuchigwa* adzalikolowola ndipo ana a chiwombankhanga adzalidya.