Machitidwe 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Paulo atawaika manja,+ mzimu woyera unafika pa iwo, ndipo anayamba kulankhula malilime ndi kunenera.+ 1 Akorinto 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala ndi chikondi, komanso pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zauzimu,+ makamaka kunenera.+
6 Ndiyeno Paulo atawaika manja,+ mzimu woyera unafika pa iwo, ndipo anayamba kulankhula malilime ndi kunenera.+
14 Yesetsani kukhala ndi chikondi, komanso pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zauzimu,+ makamaka kunenera.+