Machitidwe 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Elima, wamatsenga, (uku ndiye kumasulira kwa dzina lakeli) anayamba kutsutsana nawo.+ Iye anali kuyesetsa kuti bwanamkubwayo asakhulupirire Ambuye.
8 Koma Elima, wamatsenga, (uku ndiye kumasulira kwa dzina lakeli) anayamba kutsutsana nawo.+ Iye anali kuyesetsa kuti bwanamkubwayo asakhulupirire Ambuye.