Miyambo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Phunzitsa mwana m’njira yomuyenerera.+ Ngakhale akadzakalamba sadzapatukamo.+ Machitidwe 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.
16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.