1 Timoteyo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa chopereka malangizo awa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino+ chimene wachitsatira mosamala.+
6 Chifukwa chopereka malangizo awa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino+ chimene wachitsatira mosamala.+