Aroma 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje. Afilipi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+
13 Tiyeni tiyende moyenera+ monga usana, osati m’maphwando aphokoso ndi kumwa mwauchidakwa,*+ osati m’chiwerewere ndi khalidwe lotayirira,+ ndiponso osati m’mikangano+ ndi nsanje.
3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+