Machitidwe 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene anatsagana naye pa ulendowu anali Sopaturo+ mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe, ndi Timoteyo,+ koma ochokera m’chigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+ Aefeso 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ m’bale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika mwa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+ 2 Timoteyo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Tukiko+ ndamutuma ku Efeso.
4 Amene anatsagana naye pa ulendowu anali Sopaturo+ mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe, ndi Timoteyo,+ koma ochokera m’chigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+
21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ m’bale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika mwa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+