1 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Antchito a panyumba akhale ogonjera+ mabwana awo ndi mantha oyenera,+ osati kwa mabwana abwino ndi ololera okha, koma ngakhalenso kwa ovuta kuwakondweretsa.
18 Antchito a panyumba akhale ogonjera+ mabwana awo ndi mantha oyenera,+ osati kwa mabwana abwino ndi ololera okha, koma ngakhalenso kwa ovuta kuwakondweretsa.