Machitidwe 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki. Aheberi 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Dziwani kuti m’bale wathu Timoteyo+ wamasulidwa, ndipo ngati angabwere posachedwapa, ndibwera naye limodzi kudzakuonani.
16 Choncho Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wachiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.
23 Dziwani kuti m’bale wathu Timoteyo+ wamasulidwa, ndipo ngati angabwere posachedwapa, ndibwera naye limodzi kudzakuonani.