2 Akorinto 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 N’chifukwa chake talimbikitsidwa. Komabe, kuwonjezera pa kulimbikitsidwa, tinakondweranso kwambiri chifukwa chakuti Tito ali ndi chimwemwe, popeza nonsenu mwatsitsimutsa mtima wake.+
13 N’chifukwa chake talimbikitsidwa. Komabe, kuwonjezera pa kulimbikitsidwa, tinakondweranso kwambiri chifukwa chakuti Tito ali ndi chimwemwe, popeza nonsenu mwatsitsimutsa mtima wake.+