2 Timoteyo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero, usachite manyazi ndi ntchito yochitira umboni za Ambuye wathu,+ kapena za ineyo amene ndine mkaidi chifukwa cha iye.+ Khala wokonzeka kumva zowawa+ mu mphamvu ya Mulungu+ chifukwa cha uthenga wabwino.
8 Chotero, usachite manyazi ndi ntchito yochitira umboni za Ambuye wathu,+ kapena za ineyo amene ndine mkaidi chifukwa cha iye.+ Khala wokonzeka kumva zowawa+ mu mphamvu ya Mulungu+ chifukwa cha uthenga wabwino.