Afilipi 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 pakuti chifukwa cha ntchito ya Ambuye, anatsala pang’ono kufa.+ Anaika moyo wake pachiswe, kuti adzanditumikire m’malo mwa inu,+ popeza simuli kuno.
30 pakuti chifukwa cha ntchito ya Ambuye, anatsala pang’ono kufa.+ Anaika moyo wake pachiswe, kuti adzanditumikire m’malo mwa inu,+ popeza simuli kuno.