Akolose 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu akapolo, muzimvera ambuye anu a padziko lapansi+ pa zinthu zonse, osati mwachiphamaso ngati ofuna kukondweretsa+ anthu, koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.+
22 Inu akapolo, muzimvera ambuye anu a padziko lapansi+ pa zinthu zonse, osati mwachiphamaso ngati ofuna kukondweretsa+ anthu, koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.+