Aefeso 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 sindileka kuyamika Mulungu chifukwa cha inu. Ndikupitirizabe kukutchulani m’mapemphero anga,+ 1 Atesalonika 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nthawi zonse timayamika Mulungu tikamatchula za inu nonse m’mapemphero athu.+