Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 11:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho taona kukoma mtima+ komanso kusalekerera+ kwa Mulungu. Amene anagwa anaona kusalekerera+ kwake, koma iweyo ukuona kukoma mtima kwa Mulungu, malinga ngati ukukhalabe+ m’kukoma mtima kwake. Apo ayi, iwenso udzadulidwa.+

  • 2 Akorinto 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tsopano kudzera mwa Khristu, tikhoza kunena zimenezi molimba mtima+ pamaso pa Mulungu.

  • 1 Yohane 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tikudziwa kuti tinali akufa koma tsopano ndife amoyo+ chifukwa timakonda abale athu.+ Amene sakonda m’bale wake ndiye kuti adakali mu imfa.+

  • Chivumbulutso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena