Yohane 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko+ a dziko.+ Aefeso 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+
24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko+ a dziko.+
4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+