Genesis 31:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Atiweruze mulungu wa Abulahamu,+ mulungu wa Nahori,+ yemwe ali mulungu wa bambo awo.” Koma Yakobo analumbira pa Mulungu amene bambo ake Isaki anali kumuopa.+ Genesis 47:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yakobo anati: “Lumbira kwa ine.” Yosefe analumbira kwa iye.+ Pamenepo Isiraeli anawerama n’kutsamira kumutu kwa bedi lake.+
53 Atiweruze mulungu wa Abulahamu,+ mulungu wa Nahori,+ yemwe ali mulungu wa bambo awo.” Koma Yakobo analumbira pa Mulungu amene bambo ake Isaki anali kumuopa.+
31 Ndiyeno Yakobo anati: “Lumbira kwa ine.” Yosefe analumbira kwa iye.+ Pamenepo Isiraeli anawerama n’kutsamira kumutu kwa bedi lake.+