Genesis 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo Melekizedeki,+ mfumu ya ku Salemu,+ anabweretsa mkate ndi vinyo.+ Iyeyu anali wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+ Salimo 76:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malo ake opumulirako ali ku Salemu,+Malo ake okhalamo ali ku Ziyoni.+
18 Ndipo Melekizedeki,+ mfumu ya ku Salemu,+ anabweretsa mkate ndi vinyo.+ Iyeyu anali wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+