-
Levitiko 11:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Madzi a m’chiwiya chimenechi akagwera pachakudya chilichonse, chakudyacho chizikhala chodetsedwa. Ndipo chakumwa chilichonse chimene mungamwere m’chiwiya chilichonse, chikasakanikirana ndi madzi ochokera m’chiwiya chodetsedwa chija, chakumwacho chizikhala chodetsedwa.
-