Agalatiya 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero kodi Chilamulo chimatsutsa malonjezo a Mulungu?+ Zimenezo sizingachitike ngakhale pang’ono. Pakanaperekedwa lamulo lopatsa moyo,+ bwenzi chilungamo chikudzera m’chilamulo.+
21 Chotero kodi Chilamulo chimatsutsa malonjezo a Mulungu?+ Zimenezo sizingachitike ngakhale pang’ono. Pakanaperekedwa lamulo lopatsa moyo,+ bwenzi chilungamo chikudzera m’chilamulo.+