Salimo 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nsembe ndiponso zopereka, simunasangalale nazo.+Inu munatsegula makutu anga.+Simunapemphe nsembe yopsereza ndi nsembe yamachimo.+
6 Nsembe ndiponso zopereka, simunasangalale nazo.+Inu munatsegula makutu anga.+Simunapemphe nsembe yopsereza ndi nsembe yamachimo.+