Levitiko 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Lamulo limeneli laperekedwa kuti nsembe zimene ana a Isiraeli akuzipereka kunja,+ azibwera nazo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako kuti azipereke kwa Yehova.+ Zimenezi ziziperekedwa monga nsembe zachiyanjano kwa Yehova.+
5 Lamulo limeneli laperekedwa kuti nsembe zimene ana a Isiraeli akuzipereka kunja,+ azibwera nazo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako kuti azipereke kwa Yehova.+ Zimenezi ziziperekedwa monga nsembe zachiyanjano kwa Yehova.+