Mateyu 27:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka, ndipo matanthwe anang’ambika.+
51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka, ndipo matanthwe anang’ambika.+