Genesis 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi chilichonse chimene Sara wakhala akunena kwa iwe chokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mvera mawu ake, chifukwa amene adzatchedwa mbewu yako adzachokera mwa Isaki.+ Aroma 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso si onse amene ali ana chifukwa chongokhala mbewu ya Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+
12 Koma Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi chilichonse chimene Sara wakhala akunena kwa iwe chokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mvera mawu ake, chifukwa amene adzatchedwa mbewu yako adzachokera mwa Isaki.+
7 Ndiponso si onse amene ali ana chifukwa chongokhala mbewu ya Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+