Machitidwe 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nthawi imeneyo Mose anabadwa,+ ndipo anali wokongola kwambiri, ngakhalenso pamaso pa Mulungu.+ Mose analeredwa m’nyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu.
20 Pa nthawi imeneyo Mose anabadwa,+ ndipo anali wokongola kwambiri, ngakhalenso pamaso pa Mulungu.+ Mose analeredwa m’nyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu.