1 Akorinto 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Motero, sikuti ndikungothamanga+ osadziwa kumene ndikulowera. Mmene ndikuponyera nkhonya zanga, sikuti ndikungomenya mphepo ayi,+ Afilipi 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abale, ine sindidziyesa ngati ndalandira kale mphotoyo ayi. Koma pali chinthu chimodzi chimene ndikuchita: Ndikuiwala zinthu zakumbuyo+ ndipo ndikuyesetsa kuti ndikapeze zakutsogolo.+ 1 Petulo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero, lekani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka ndi mtundu uliwonse wa miseche.+
26 Motero, sikuti ndikungothamanga+ osadziwa kumene ndikulowera. Mmene ndikuponyera nkhonya zanga, sikuti ndikungomenya mphepo ayi,+
13 Abale, ine sindidziyesa ngati ndalandira kale mphotoyo ayi. Koma pali chinthu chimodzi chimene ndikuchita: Ndikuiwala zinthu zakumbuyo+ ndipo ndikuyesetsa kuti ndikapeze zakutsogolo.+
2 Chotero, lekani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka ndi mtundu uliwonse wa miseche.+