Deuteronomo 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwana wapathengo+ asalowe mumpingo wa Yehova. Ana ake asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10.
2 “Mwana wapathengo+ asalowe mumpingo wa Yehova. Ana ake asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10.