1 Atesalonika 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani. Aheberi 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mundiperekere moni kwa onse amene akutsogolera pakati panu,+ ndiponso kwa oyera ena onse. A ku Italiya+ akukupatsani moni.
12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani.
24 Mundiperekere moni kwa onse amene akutsogolera pakati panu,+ ndiponso kwa oyera ena onse. A ku Italiya+ akukupatsani moni.