Salimo 79:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ife, anthu anu, nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Tidzakutamandani ku mibadwomibadwo.+ Yohane 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Yesu anawauzanso kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Ine ndine khomo+ la nkhosa.
13 Koma ife, anthu anu, nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Tidzakutamandani ku mibadwomibadwo.+