Afilipi 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti Mulungu amachita zinthu m’njira imene imamusangalatsa. Iye amalimbitsa zolakalaka zanu+ kuti muchite zinthu zonse zimene iye amakonda.+ 2 Atesalonika 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 alimbikitse mitima yanu ndi kukulimbikitsani muntchito yabwino iliyonse ndiponso m’mawu.+
13 Pakuti Mulungu amachita zinthu m’njira imene imamusangalatsa. Iye amalimbitsa zolakalaka zanu+ kuti muchite zinthu zonse zimene iye amakonda.+