Mateyu 13:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi? Machitidwe 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma iye anawakwezera dzanja+ kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova anamutulutsira m’ndende. Kenako iye anati: “Zinthu zimenezi mukazifotokoze kwa Yakobo+ ndi kwa abale.” Atatero anatuluka n’kupita kumalo ena. Agalatiya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma sindinaone mtumwi winanso kupatulapo Yakobo,+ m’bale+ wa Ambuye.
55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?
17 Koma iye anawakwezera dzanja+ kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova anamutulutsira m’ndende. Kenako iye anati: “Zinthu zimenezi mukazifotokoze kwa Yakobo+ ndi kwa abale.” Atatero anatuluka n’kupita kumalo ena.