Maliko 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kumeneko anatulutsa ziwanda zambiri,+ ndi kudzoza mafuta anthu ambiri odwala+ ndi kuwachiritsa.+