1 Mafumu 18:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ahabu anapitadi kukadya ndi kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli. Ndiyeno anakhala chogwada+ ataika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+ 1 Mafumu 18:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+
42 Ahabu anapitadi kukadya ndi kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli. Ndiyeno anakhala chogwada+ ataika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+
45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+