Salimo 115:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+ Aroma 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+ 1 Akorinto 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala ndi chikondi, komanso pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zauzimu,+ makamaka kunenera.+
23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+
14 Yesetsani kukhala ndi chikondi, komanso pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zauzimu,+ makamaka kunenera.+