Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 136:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Yamikani wopanga zounikira zazikulu:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Yesaya 45:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+ Ndimabweretsa mtendere+ ndiponso tsoka.+ Ine Yehova ndimapanga zonsezi.+

  • Yesaya 60:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Dzuwa lako silidzalowanso, ndipo mwezi wako sudzapitanso kumdima. Pakuti kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+

  • Aefeso 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pakuti poyamba munali mdima,+ koma tsopano ndinu kuwala+ mogwirizana ndi Ambuye. Yendanibe ngati ana a kuwala.

  • 1 Yohane 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Umenewu ndi uthenga umene taumva kuchokera kwa iye ndipo tikuulengeza kwa inu,+ kuti Mulungu ndiye kuwala+ ndipo mwa iye mulibe mdima ngakhale pang’ono.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena