Luka 6:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Nanga n’chifukwa chiyani mumandiitana kuti ‘Ambuye! Ambuye!’ koma osachita zimene ndimanena?+ Yakobo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Abale anga, kodi pali phindu lanji ngati wina amati ali ndi chikhulupiriro+ koma sachita ntchito zake?+ Kodi chikhulupiriro chimenecho chingamupulumutse?+
14 Abale anga, kodi pali phindu lanji ngati wina amati ali ndi chikhulupiriro+ koma sachita ntchito zake?+ Kodi chikhulupiriro chimenecho chingamupulumutse?+