Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 31:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ngati ndinkaona munthu akuzunzika chifukwa chosowa chovala,+

      Kapena kuona kuti wosauka alibe chofunda,

  • Yesaya 58:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+

  • Mateyu 25:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ndinali wamaliseche+ koma inu munandiveka. Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali m’ndende+ koma inu munabwera kudzandiona.’

  • Luka 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Poyankha iye anali kuwauza kuti: “Munthu amene ali ndi malaya awiri amkati agawireko munthu amene alibiretu. Amenenso ali ndi chakudya achite chimodzimodzi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena