Machitidwe 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire+ kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira wakuti iyeyu ndi Amene Mulungu anamuika kukhala woweruza anthu amoyo ndi akufa.+ 2 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamaso pa Mulungu ndi pa Khristu Yesu, amene anaikidwiratu kudzaweruza+ amoyo ndi akufa,+ akadzaonekera+ bwinobwino ndiponso akadzabwera mu ufumu wake,+ ndikukulamula mwamphamvu kuti,
42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire+ kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira wakuti iyeyu ndi Amene Mulungu anamuika kukhala woweruza anthu amoyo ndi akufa.+
4 Pamaso pa Mulungu ndi pa Khristu Yesu, amene anaikidwiratu kudzaweruza+ amoyo ndi akufa,+ akadzaonekera+ bwinobwino ndiponso akadzabwera mu ufumu wake,+ ndikukulamula mwamphamvu kuti,