Machitidwe 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda, ali osangalala+ chifukwa chakuti Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.+ Yakobo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abale anga, sangalalani pamene mukukumana ndi mayesero osiyanasiyana,+
41 Choncho atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda, ali osangalala+ chifukwa chakuti Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.+