1 Akorinto 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiponso, munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa+ pa zinthu zonse. Iwo amachita zimenezo kuti apeze nkhata ya kumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata ya kumutu yosakhoza kuwonongeka.+ 1 Petulo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+
25 Ndiponso, munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa+ pa zinthu zonse. Iwo amachita zimenezo kuti apeze nkhata ya kumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata ya kumutu yosakhoza kuwonongeka.+
4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+