Aroma 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi amaika maganizo awo pa zinthu za thupi,+ koma otsatira za mzimu amaika maganizo awo pa zinthu za mzimu.+ Agalatiya 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+ Yakobo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi nkhondo zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Nanga kukangana pakati panu kukuchokera kuti? Kodi sizikuchokera m’zilakolako za thupi lanu+ zimene zikuchita nkhondo m’ziwalo zanu?+
5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi amaika maganizo awo pa zinthu za thupi,+ koma otsatira za mzimu amaika maganizo awo pa zinthu za mzimu.+
24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+
4 Kodi nkhondo zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Nanga kukangana pakati panu kukuchokera kuti? Kodi sizikuchokera m’zilakolako za thupi lanu+ zimene zikuchita nkhondo m’ziwalo zanu?+